Yeremiya 24:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapatsa iwo mtima wakundidziwa, kuti ndine Yehova; nadzakhala anthu anga, ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wao; pakuti adzabwera kwa Ine ndi mtima wao.

Yeremiya 24

Yeremiya 24:1-10