Yeremiya 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtanga umodzi unali ndi nkhuyu zabwinobwino, ngati nkhuyu zoyamba kuca; ndipo mtanga umodzi unali ndi nkhuyu zoipaipa, zosadyeka, zinali zoipa.

Yeremiya 24

Yeremiya 24:1-5