Yeremiya 23:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma, Pali Yehova, amene anakweza ndi kutsogolera mbeu za nyumba ya Israyeli kuwaturutsa m'dziko la kumpoto, ndi ku maiko onse kumene ndinawapitikitsirako, ndipo adzakhala m'dziko lao.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:1-13