Yeremiya 23:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, masiku alinkudza, ati Yehova, ndidzamuukitsira Davide Mphukira wolungama, ndipo Iye adzakhala Mfumu, adzacita mwanzeru, nadzacita ciweruzo ndi cilungamo m'dziko lino.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:2-10