Yeremiya 23:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi munthu angathe kubisala mobisika kuti ndisamuone iye? ati Yehova. Kodi Ine sindidzala kumwamba ndi dziko lapansi? ati Yehova.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:21-26