Yeremiya 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova wa makamu atero za aneneri: Taonani, ndidzadyetsa iwo cowawa, ndidzamwetsa iwo madzi andulu; pakuti kwa aneneri a ku Yerusalemu kuipitsa kwaturukira kunka ku dziko lonse.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:9-24