Yeremiya 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati mudzacitadi ici pamenepo, padzalowa pa zipata za nyumba iyi mafumu okhala pa mpando wacifumu wa Davide, okwera m'magareta ndi pa akavalo, iye, ndi atumiki ace, ndi anthu ace.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:1-11