Yeremiya 22:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe wokhala m'Lebano, womanga cisa cako m'mikungudza, udzacitidwa cisoni cacikuru nanga pamene mapweteko adzadza kwa iwe, monga mkazi alinkudwala!

Yeremiya 22

Yeremiya 22:13-29