Yeremiya 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamlirire wakufa, musacite maliro ace; koma mumliritse iye amene amuka, pakuti sadzabweranso, kapena kuonanso dziko la kwao.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:3-15