Yeremiya 21:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine mwini ndidzamenyana ndi inu ndi dzanja lotambasuka ndi mkono wamphamvu, m'mkwiyo, ndi m'kupsya mtima, ndi m'ukali waukuru.

Yeremiya 21

Yeremiya 21:1-12