Yeremiya 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa Maseya wansembe, akati,

Yeremiya 21

Yeremiya 21:1-5