Yeremiya 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Pasuri anampanda Yeremiya mneneriyo, namuika matangadza amene anali m'cipata ca kumtunda ca Benjamini, cimene cinali ku nyumba ya Yehova.

Yeremiya 20

Yeremiya 20:1-6