Yeremiya 20:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa sanandipha ine m'mimba; kuti mai wanga akhale manda anga, ndi mimba yace yaikuru nthawi zonse.

Yeremiya 20

Yeremiya 20:15-18