Yeremiya 2:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbadwo inu, taonani mau a Yehova. Kodi ndakhala kwa Israyeli cipululu? Kapena dziko la mdima woti bii? Cifukwa ninji ati anthu anga, Tamasuka sitidzabweranso konse kwa Inu?

Yeremiya 2

Yeremiya 2:27-37