Yeremiya 2:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Bwanji uti, Sindinaipitsidwa, sindinatsata Abaala? Ona njira yako m'cigwa, dziwa cimene wacicita; ndiwe ngamila yothamanga yoyenda m'njira zace;

Yeremiya 2

Yeremiya 2:17-31