Yeremiya 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nuziti kwa iwo, Yehova wa makamu atero: Comweco ndidzaphwanya anthu awa ndi mudzi uwu, monga aphwanya mbiya ya woumba, imene sangathe kulumbanso, ndipo adzaika maliro m'Tofeti, mpaka mulibe malo akuikamo.

Yeremiya 19

Yeremiya 19:4-12