Yeremiya 18:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi coipa cibwezedwe pa cabwino? pakuti akumbira moyo wanga dzenje, Mukumbukire kuti ndinaima pamaso panu kuwanenera zabwino, kuwacotsera iwo ukali wanu.

Yeremiya 18

Yeremiya 18:15-23