Yeremiya 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakhala ngati tsanya la m'cipululu, ndipo saona pamene cifika cabwino; koma adzakhala m'malo oumitsa m'cipululu, dziko lacikungu lopanda anthu.

Yeremiya 17

Yeremiya 17:1-8