Yeremiya 17:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati simudzamvera Ine kulipatula tsiku la Sabata, kusanyamula katundu ndi kulowa pa zipata za Yerusalemu tsiku la Sabata; pamenepo ndidzayatsa moto m'zipata zacezo, ndipo udzatha zinyumba za Yerusalemu, osazimidwanso.

Yeremiya 17

Yeremiya 17:18-27