Yeremiya 17:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala, ngati mu ndimveretsa Ine, ati Yehova, kuti musalowetse katundu pa zipata za mudzi uwu tsiku la Sabata, koma mupatule tsiku la Sabata, osagwira nchito m'menemo;

Yeremiya 17

Yeremiya 17:23-27