Yeremiya 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine, pokhala mbusa sindinafulumira kucokerako kuti ndikutsateni Inu; sindinakhumba tsiku la tsoka; Inu mudziwa, cimene cinaturuka pa milomo yanga cinali pamaso panu.

Yeremiya 17

Yeremiya 17:10-23