Yeremiya 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga nkhwali iumatira pa mazira amene sinaikira, momwemo iye amene asonkhanitsa cuma, koma mosalungama; pakati pa masiku ace cidzamsiya iye, ndipo pa citsirizo adzakhala wopusa.

Yeremiya 17

Yeremiya 17:8-20