Yeremiya 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli; Taonani, ndidzaletsa pano, pamaso panu masiku anu, mau akukondwerera ndi mau akusangalala, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi.

Yeremiya 16

Yeremiya 16:1-11