Yeremiya 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amasiye ao andicurukira Ine kopambana mcenga wa kunyanja; ndatengera wofunkha usana afunkhire mai wao wa anyamata; ndamgwetsera dzidzidzi kuwawa mtima ndi mantha.

Yeremiya 15

Yeremiya 15:1-10