Yeremiya 15:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaika pa iwo mitundu inai, ati Yehova, lupanga lakupha, agaru akung'amba, mbalame za m'mlengalenga, ndi zirombo zapansi, zakulusa ndi kuononga.

Yeremiya 15

Yeremiya 15:1-5