Yeremiya 15:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzakuyesa iwe linga lamkuwa la anthu awa; ndipe adzamenyana ndi iwe, koma iwo sadzakuposa iwe; pakuti Ine ndiri ndi iwe kuti ndikupulumutse ndi kukulanditsa iwe, ati Yehova.

Yeremiya 15

Yeremiya 15:10-21