Yeremiya 15:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kupweteka kwanga kuti cipwetekere bwanji, ndi bala langa losapoleka, likana kupola? kodi mudzakhala kwa ine ngati kamtsinje konyenga, ngati madzi omwerera?

Yeremiya 15

Yeremiya 15:10-20