Yeremiya 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova za aneneri onenera m'dzina langa, ndipo sindinawatuma, koma ati, Lupanga ndi cirala sizidzakhala m'dziko muno; ndi lupanga ndi cirala aneneriwo adzathedwa.

Yeremiya 14

Yeremiya 14:12-17