Yeremiya 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinati, Ha, Ambuye Yehova! taonani, aneneri ati kwa iwo, Simudzaona lupanga, simudzakhala ndi cirala; koma ndidzakupatsani mtendere weniweni mommuno.

Yeremiya 14

Yeremiya 14:3-14