Yeremiya 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali atapita masiku ambiri, kuti Yehova anati kwa ine, Uka, pita ku Firate, nukatenge kumeneko mpango uja, ndinakuuza iwe ukaubise kumeneko.

Yeremiya 13

Yeremiya 13:1-14