Yeremiya 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati simudzamva, moyo wanga udzalira m'tseri cifukwa ca kunyada kwanu; diso langa lidzalira kwambiri, lidzagwa misozi, cifukwa zoweta za Yehova zagwidwa m'nsinga.

Yeremiya 13

Yeremiya 13:13-20