Yeremiya 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu oipa awa, amene akana kumva mau anga, amene ayenda m'kuumirira kwa mtima wao, atsata milungu yina kuitumikira, ndi kuigwadira, adzakhala ngati mpango uwu, wosayenera kanthu.

Yeremiya 13

Yeremiya 13:8-19