Yeremiya 11:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndinatsimikizitsa kwa atate anu tsiku lomwe ndinawaturutsa iwo ku dziko la Aigupto, mpaka lero lomwe, kuuka mamawa ndi kutsimikiza, kuti, Mverani mau anga.

Yeremiya 11

Yeremiya 11:2-12