Yeremiya 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti ndikalimbikitse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu, ndiwapatse dziko mayenda mkaka ndi uci, monga lero lomwe. Ndipo ndinayankha, ndi kuti, Amen, Yehova.

Yeremiya 11

Yeremiya 11:1-15