Yeremiya 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma, Yehova wa makamu, amene aweruza molungama, pamene ayesa imso ndi mtima, ndikuoneni Inu mulikuwabwezera cilango, pakuti kwa Inu ndaulula mlandu wanga.

Yeremiya 11

Yeremiya 11:10-23