Yeremiya 10:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbiri yamveka, taonani ikudza, ndi phokoso lalikuru lituruka m'dziko la kumpoto, likacititse midzi ya Yuda bwinja, ndi mbuto ya nkhandwe.

Yeremiya 10

Yeremiya 10:12-25