Yeremiya 10:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hema wanga waonongeka, zingwe zanga zonse zaduka; ana anga aturuka mwa ine, palibe iwo; palibenso amene adzamanga hema wanga, kapena kucinga nsaru zanga,

Yeremiya 10

Yeremiya 10:15-23