Yakobo 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, lezani mtima, abale, kufikira kudza kwace kwa Ambuye. Taonani, wolima munda alindira cipatso cofunikatu ca dziko, ndi kuleza mtima naco kufikira cikalandira mvula ya myundo ndi masika,

Yakobo 5

Yakobo 5:1-12