Yakobo 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abale anga, ngati wina wa inu asocera posiyana ndi coonadi, ndipo ambweza iye mnzace;

Yakobo 5

Yakobo 5:15-20