Yakobo 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pali wina kodi adwala mwa inu? Adziitanire akuru a Mpingo, ndipo apemphere pa iye, atamdzoza ndi mafuta m'dzina la Ambuye:

Yakobo 5

Yakobo 5:6-16