Yakobo 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo lilime ndilo moto; ngati dziko la cosalungama mwa ziwalo zathu laikika lilime, ndili lodetsa thupi lonse, niliyatsa mayendedwe a cibadwidwe, ndipo liyatsidwa ndi gehena.

Yakobo 3

Yakobo 3:1-15