Yakobo 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma apemphe ndi cikhulupiriro, wosakayika konse; pakuti wokayikayo afanana ndi pfunde la nyanja lotengeka ndi mphepo ndi kuwinduka nayo.

Yakobo 1

Yakobo 1:1-12