Yakobo 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cipiriro cikhale nayo nchito yace yangwiro, kuti mukakhale angwiro ndi opanda cirema, osasowa kanthu konse.

Yakobo 1

Yakobo 1:1-5