Yakobo 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mphatso iri yonse yabwino, ndi cininkho ciri conse cangwiro zicokera Kumwamba, zotsika kwa Atate wa mauniko, amene alibe cisanduliko, kapena mthunzi wa citembenukiro.

Yakobo 1

Yakobo 1:14-22