Tito 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Okhulupirika mauwa, ndipo za izi ndifuna kuti ulimbitse mau, kuti iwo akukhulupirira Mulungu asamalire akhalebe atsogoleri a nchito zabwino. Izi nzokoma ndi zopindulitsa anthu;

Tito 3

Tito 3:6-15