Tito 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene anadzipereka yekha m'malo mwa ife, kuti akatiombole Ife ku zoipa zonse, nakadziyeretsere yekha anthu akhale ace eni eni, acangu pa nchito zokoma.

Tito 2

Tito 2:4-15