Rute 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maso ako akhale pa munda acekawo, ndi kuwatsata; kodi sindinawauza anyamata asakukhudze? Ndipo ukamva ludzu, muka kumitsuko, ukamweko otunga anyamatawo,

Rute 2

Rute 2:6-10