Rute 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rute Mmoabu anati, Ananenanso nane ndithu, Uwaumirire anyamata anga, mpaka atatha kuceka zanga zonse za m'minda.

Rute 2

Rute 2:18-22