Rute 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Mundikomere mtima mbuye wanga, popeza mwandisangalatsa, popezanso mwanena cokondweretsa mtima wa mdzakazi wanu, ndingakhale ine sindine ngati mmodzi wa adzakazi anu.

Rute 2

Rute 2:5-18