Rute 1:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anabwera Naomi ndi Rute Mmoabu mpongozi wace pamodzi naye, amene anabwera kucokera ku dziko la Moabu; ndipo anafika ku Betelehemu, pakuyamba anthu kuceka barele.

Rute 1

Rute 1:14-22